Reader ready.
CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO (Book - Nyanja)
Cholinga cha bukhuli ndi kuwaunikira anthu omwe amafuna kudziwa zoona zokhazokha, pa zauthenga weniweni womwe Yesu (mtendere ukhale pa iye) ankaphunzitsa. Bukhuli likukamba za machitidwe ena omwe analetsedwa kapena kuvomerezedwa m’Baibulo. Pali chikhulupiliro chakuti anthu akawerenga bukhuli adzipezera okha gulu lenileni la anthu lomwe limatsatira chiphunzitso cha Yesu (mtendere ukhale pa iye). Umboni wochokera m’Baibulo ugwiritsidwa ntchito pofuna kuwaunikira awerengi athu chipembedzo chenicheni cha Yesu (mtendere ukhale pa iye) lero lino. Anthuwa ayenera kudziwa otsatira enieni a chiphunzitso cha Baibulo.
Download all material files
2 files • 1 MB
Material files
1 / 2Social-friendly share text
Ndine wokondwa kugawana izi nanu:
📘 CHUMA CHOBISIKA M’BAIBULO (Nyanja)
📝 Cholinga cha bukhuli ndi kuwaunikira anthu omwe amafuna kudziwa zoona zokhazokha, pa zauthenga weniweni womwe Yesu (mtendere ukhale pa iye) ankaphunzitsa. Bukhuli likukamba za machitidwe ena omwe analetsedwa kapena kuvomerezedwa m’Baibulo. Pali chikhulupiliro chakuti anthu akawerenga bukhuli adzipezera okha gulu lenileni la anthu lomwe limatsatira chiphunzitso cha Yesu (mtendere ukhale pa iye). Umboni wochokera m’Baibulo ugwiritsidwa ntchito pofuna kuwaunikira awerengi athu chipembedzo chenicheni cha Yesu (mtendere ukhale pa iye) lero lino. Anthuwa ayenera kudziwa otsatira enieni a chiphunzitso cha Baibulo.
🔗 https://b.islamhouse.com/ny/books/2831536